An artist, author, theologian, and musician, Siku is the international bestselling graphic novelist of The Manga Bible and one of Britain's leading comic book/concept artists, having worked for 2000AD, producing titles such as Judge Dredd, Slaine, and his co-creation, Pan-African Judges.His...
“ ‘Mwala umene omanga nyumba anawukana wasanduka mwala wa pa ngodya. 18Aliyense amene agwa pa mwalawu adzapweteka, koma iye amene udzamugwera udzamuphwanya.’ ” 19Aphunzitsi amalamulo ndi akulu a ansembe amafuna njira yoti amuphe nthawi yomweyo, chifukwa anadziwa kuti...
Kudwala kwa Hezekiya - Masiku amenewo Hezekiya anadwala ndipo anali pafupi kufa. Mneneri Yesaya, mwana wa Amozi anapita kukamuona ndipo anamuwuza