Ibweretu ngati ingathe kukupulumutsani pamene muli pamavuto!Inu anthu a ku Yuda, milungu yanu ndi yambiri kuchuluka kwake ngati mizinda yanu.29 “Kodi mukundizengeranji mlandu? Nonse mwandiwukira,” akutero Yehova.30 “Ine ndinalanga anthu ako popanda phindu; iwo sanaphunzirepo ...